Mateyu 5:39, 40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma ine ndikukuuzani kuti: Musamalimbane ndi munthu woipa, koma wina akakumenyani mbama patsaya lakumanja, muzimupatsanso tsaya linalo.+ 40 Ngati munthu akufuna kukutengera kukhoti kuti akulande malaya ako amkati, uzimupatsanso akunja.+
39 Koma ine ndikukuuzani kuti: Musamalimbane ndi munthu woipa, koma wina akakumenyani mbama patsaya lakumanja, muzimupatsanso tsaya linalo.+ 40 Ngati munthu akufuna kukutengera kukhoti kuti akulande malaya ako amkati, uzimupatsanso akunja.+