Aefeso 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa mfundo iyi mukuidziwa ndipo mukuimvetsa bwino, kuti munthu wachiwerewere*+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndi kulambira mafano, sadzalowa mu Ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+ Chivumbulutso 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kunja kuli anthu amene ali ngati agalu* komanso amene amachita zamizimu, achiwerewere,* opha anthu, olambira mafano ndi aliyense amene amakonda kunama komanso kuchita zachinyengo.’+
5 Chifukwa mfundo iyi mukuidziwa ndipo mukuimvetsa bwino, kuti munthu wachiwerewere*+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndi kulambira mafano, sadzalowa mu Ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+
15 Kunja kuli anthu amene ali ngati agalu* komanso amene amachita zamizimu, achiwerewere,* opha anthu, olambira mafano ndi aliyense amene amakonda kunama komanso kuchita zachinyengo.’+