Genesis 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa cha zimenezi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake nʼkudziphatika kwa mkazi wake* ndipo iwo adzakhala thupi limodzi.+ Aheberi 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posadetsedwa,+ chifukwa Mulungu adzaweruza achiwerewere* ndiponso achigololo.+
24 Chifukwa cha zimenezi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake nʼkudziphatika kwa mkazi wake* ndipo iwo adzakhala thupi limodzi.+
4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posadetsedwa,+ chifukwa Mulungu adzaweruza achiwerewere* ndiponso achigololo.+