Machitidwe 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwo atamva zimenezi anayamba kutamanda Mulungu, komabe anamuuza kuti: “Mʼbale, pali Ayuda ambiri okhulupirira ndipo onsewa ndi odzipereka pa nkhani yotsatira Chilamulo.+
20 Iwo atamva zimenezi anayamba kutamanda Mulungu, komabe anamuuza kuti: “Mʼbale, pali Ayuda ambiri okhulupirira ndipo onsewa ndi odzipereka pa nkhani yotsatira Chilamulo.+