Malaki 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa ine ndimadana ndi zoti anthu azithetsa mabanja,”+ watero Yehova Mulungu wa Isiraeli. “Ndimadana ndi munthu wankhanza.* Samalani kuti mukhale ndi maganizo oyenera ndipo musamachite zachinyengo,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Mateyu 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Moti sakhalanso kuti ndi awiri, koma thupi limodzi. Choncho chimene Mulungu wachimanga pamodzi,* munthu asachilekanitse.”+ Aefeso 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Komabe, aliyense wa inu azikonda mkazi wake+ ngati mmene amadzikondera yekha komanso mkazi azilemekeza kwambiri mwamuna wake.+
16 Chifukwa ine ndimadana ndi zoti anthu azithetsa mabanja,”+ watero Yehova Mulungu wa Isiraeli. “Ndimadana ndi munthu wankhanza.* Samalani kuti mukhale ndi maganizo oyenera ndipo musamachite zachinyengo,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
6 Moti sakhalanso kuti ndi awiri, koma thupi limodzi. Choncho chimene Mulungu wachimanga pamodzi,* munthu asachilekanitse.”+
33 Komabe, aliyense wa inu azikonda mkazi wake+ ngati mmene amadzikondera yekha komanso mkazi azilemekeza kwambiri mwamuna wake.+