Malaki 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga? Ndiye nʼchifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo+ nʼkumaipitsa pangano la makolo athu akale? Mateyu 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso musamatchule aliyense kuti atate wanu padziko lapansi pano, chifukwa Atate+ wanu ndi mmodzi Yekhayo, amene amakhala kumwamba.
10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga? Ndiye nʼchifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo+ nʼkumaipitsa pangano la makolo athu akale?
9 Komanso musamatchule aliyense kuti atate wanu padziko lapansi pano, chifukwa Atate+ wanu ndi mmodzi Yekhayo, amene amakhala kumwamba.