Machitidwe 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene iwo ankatumikira Yehova* ndiponso kusala kudya, mzimu woyera unawauza kuti: “Mundipatulire Baranaba ndi Saulo+ kuti agwire ntchito imene ndinawaitanira.”+
2 Pamene iwo ankatumikira Yehova* ndiponso kusala kudya, mzimu woyera unawauza kuti: “Mundipatulire Baranaba ndi Saulo+ kuti agwire ntchito imene ndinawaitanira.”+