Yesaya 40:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye amapereka mphamvu kwa munthu wotopaNdipo munthu amene alibe mphamvu amamupatsa mphamvu zambiri.+ Afilipi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa Mulungu amene amandipatsa mphamvu zimene ndikufunikira.+
29 Iye amapereka mphamvu kwa munthu wotopaNdipo munthu amene alibe mphamvu amamupatsa mphamvu zambiri.+
13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa Mulungu amene amandipatsa mphamvu zimene ndikufunikira.+