-
Ezekieli 41:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 guwa lansembe lamatabwa+ limene linali mikono itatu kuchokera pansi kufika pamwamba ndipo mulitali mwake linali mikono iwiri. Guwalo linali ndi zochirikizira mʼmakona ndipo pansi pake* ndiponso mʼmbali mwake munali mwamatabwa. Ndiyeno munthu uja anandiuza kuti: “Ili ndi tebulo limene lili pamaso pa Yehova.”+
-