Yoweli 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zimenezi zikadzachitika ndidzapereka* mzimu wanga+ kwa chamoyo chilichonse,Ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzalosera.Amuna achikulire adzalota maloto,Ndipo anyamata adzaona masomphenya.+ Machitidwe 21:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku lotsatira tinanyamuka nʼkukafika ku Kaisareya ndipo tinapita kunyumba kwa mlaliki wina dzina lake Filipo. Iyeyu anali mmodzi wa amuna 7+ a mbiri yabwino aja, ndipo tinakhala naye. 9 Filipo anali ndi ana aakazi 4 osakwatiwa,* amene ankanenera.+
28 Zimenezi zikadzachitika ndidzapereka* mzimu wanga+ kwa chamoyo chilichonse,Ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzalosera.Amuna achikulire adzalota maloto,Ndipo anyamata adzaona masomphenya.+
8 Tsiku lotsatira tinanyamuka nʼkukafika ku Kaisareya ndipo tinapita kunyumba kwa mlaliki wina dzina lake Filipo. Iyeyu anali mmodzi wa amuna 7+ a mbiri yabwino aja, ndipo tinakhala naye. 9 Filipo anali ndi ana aakazi 4 osakwatiwa,* amene ankanenera.+