1 Akorinto 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikuona ngati Mulungu waika atumwife kumapeto pachionetsero ngati anthu okaphedwa,+ chifukwa zili ngati tili mʼbwalo lamasewera ndipo tikuonetsedwa kudziko,+ kwa angelo ndiponso kwa anthu.
9 Ndikuona ngati Mulungu waika atumwife kumapeto pachionetsero ngati anthu okaphedwa,+ chifukwa zili ngati tili mʼbwalo lamasewera ndipo tikuonetsedwa kudziko,+ kwa angelo ndiponso kwa anthu.