2 Akorinto 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika kapena mokakamizika,+ chifukwa Mulungu amakonda munthu amene amapereka mosangalala.+
7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika kapena mokakamizika,+ chifukwa Mulungu amakonda munthu amene amapereka mosangalala.+