1 Akorinto 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Aliyense asamangofuna zopindulitsa iyeyo basi, koma zopindulitsanso ena.+ Afilipi 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musamaganizire zofuna zanu zokha,+ koma muziganiziranso zofuna za ena.+