1 Akorinto 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Khristu sananditume kuti ndizibatiza anthu, koma kuti ndizilengeza uthenga wabwino,+ osati mwa luso la kulankhula,* kuopera kuti mtengo wozunzikirapo* wa Khristu ungakhale wopanda ntchito.
17 Khristu sananditume kuti ndizibatiza anthu, koma kuti ndizilengeza uthenga wabwino,+ osati mwa luso la kulankhula,* kuopera kuti mtengo wozunzikirapo* wa Khristu ungakhale wopanda ntchito.