-
Machitidwe 18:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Kenako Paulo anachoka ku Atene nʼkupita ku Korinto.
-
-
Machitidwe 18:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Choncho anakhala kumeneko chaka ndi miyezi 6, akuwaphunzitsa mawu a Mulungu.
-