Genesis 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Adamu ali ndi zaka 130, anabereka mwana wamwamuna wofanana naye ndipo anamʼpatsa dzina lakuti Seti.+
3 Adamu ali ndi zaka 130, anabereka mwana wamwamuna wofanana naye ndipo anamʼpatsa dzina lakuti Seti.+