2 Akorinto 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipotu, ife amene tili mutenti ino tikubuula komanso tikulemedwa, osati chifukwa chofuna kuivula, koma kuti tivale nyumba inayo,+ nʼcholinga choti thupi loti lingathe kufali lilowedwe mʼmalo ndi moyo.+
4 Ndipotu, ife amene tili mutenti ino tikubuula komanso tikulemedwa, osati chifukwa chofuna kuivula, koma kuti tivale nyumba inayo,+ nʼcholinga choti thupi loti lingathe kufali lilowedwe mʼmalo ndi moyo.+