Yohane 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mthandiziyo akadzabwera, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani mʼchoonadi chonse. Chifukwa sadzalankhula zongoganiza payekha, koma adzalankhula zimene wamva ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+
13 Koma mthandiziyo akadzabwera, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani mʼchoonadi chonse. Chifukwa sadzalankhula zongoganiza payekha, koma adzalankhula zimene wamva ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+