-
2 Akorinto 3:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Sitinganene kuti ndife oyenera kugwira ntchito imeneyi chifukwa cha mphamvu zathu, koma ndife oyenera kugwira ntchitoyi chifukwa cha Mulungu,+ 6 ndipo iyeyo anationa kuti ndife oyenera kukhala atumiki a pangano latsopano,+ osati kudzera mʼmalamulo olembedwa,+ koma kudzera mu mzimu. Malamulo olembedwa amaweruza munthu kuti afe,+ koma mzimu umapatsa munthu moyo.+
-