Yobu 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye amachititsa kuti anzeru agwere mʼmisampha yawo,+Kuti mapulani a anthu ochenjera alephereke.