1 Akorinto 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikutanthauza kuti, ena mwa inu akumanena kuti: “Ine ndine wa Paulo,” ena akuti, “Ine ndine wa Apolo,”+ enanso akuti, “Ine ndine wa Kefa,”* pamene ena akuti, “Ine ndine wa Khristu.”
12 Ndikutanthauza kuti, ena mwa inu akumanena kuti: “Ine ndine wa Paulo,” ena akuti, “Ine ndine wa Apolo,”+ enanso akuti, “Ine ndine wa Kefa,”* pamene ena akuti, “Ine ndine wa Khristu.”