-
Afilipi 4:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndikudziwa mmene zimakhalira ukakhala ndi zinthu zochepa+ komanso mmene umasangalalira ukakhala ndi zochuluka. Pa chilichonse komanso pa zochitika zosiyanasiyana, ndaphunzira chinsinsi chokhala wokhuta ndi chokhala wanjala. Ndaphunziranso chinsinsi chokhala ndi zochuluka komanso chokhala wopanda kalikonse.
-