-
Aroma 15:30-32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Choncho abale, ndikukupemphani kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu komanso chikondi cha mzimu, kuti muzilimbikira kundipempherera kwa Mulungu ndipo nanenso ndikulimbikira kupemphera.+ 31 Tilimbikire kupemphera kuti ndikapulumutsidwe+ kwa anthu osakhulupirira a ku Yudeya ndiponso kuti oyera a ku Yerusalemu akalandire bwino mphatso imene ndatenga.+ 32 Ngati Mulungu angalole, ndidzabwera kwa inu mosangalala ndipo tidzalimbikitsana.
-