Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Yesu anawayankha kuti: “Anzake a mkwati+ safunika kusala kudya ngati mkwatiyo ali nawo limodzi, si choncho kodi? Ngati mkwatiyo ali nawo limodzi sangasale kudya.

  • Aefeso 5:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 chifukwa mwamuna ndi mutu wa mkazi wake+ mofanana ndi Khristu amene ndi mutu wa mpingo,+ popeza iye ndi mpulumutsi wa thupi* limeneli.

  • Chivumbulutso 21:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndinaonanso mzinda woyera, Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu+ ndipo unali utakonzedwa ngati mkwatibwi amene wavala zokongola kuti akalandire mwamuna wake.+

  • Chivumbulutso 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mmodzi wa angelo 7 aja, amene anali ndi mbale 7 zodzaza ndi miliri 7 yotsiriza+ anabwera nʼkundiuza kuti: “Bwera kuno ndikuonetse mkwatibwi, mkazi wa Mwanawankhosa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena