Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Agalatiya 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Komabe, ngati ifeyo kapena mngelo wochokera kumwamba angalengeze nkhani ina kwa inu nʼkumanena kuti akulengeza uthenga wabwino, koma nkhaniyo nʼkukhala yosiyana ndi uthenga wabwino umene tinaulengeza kwa inu, ameneyo akhale wotembereredwa.

  • 2 Atesalonika 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma kukhalapo kwa wosamvera malamuloyo kukutheka ndi mphamvu za Satana.+ Iye akuchita ntchito iliyonse yamphamvu, zizindikiro zabodza, zodabwitsa+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena