-
1 Yohane 2:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Koma inuyo, Mulungu anakudzozani ndi mzimu wake+ ndipo mzimu umenewo udakali mwa inu, moti simukufunikira wina aliyense woti azikuphunzitsani. Koma kudzozedwako kukukuphunzitsani zinthu zonse+ ndipo ndi koona osati konama. Monga mmene kudzozedwako kwakuphunzitsirani, pitirizani kukhala ogwirizana naye.+
-