-
2 Akorinto 6:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Koma tikusonyeza mʼnjira iliyonse kuti ndife atumiki a Mulungu.+ Tikuchita zimenezi popirira zinthu zambiri, pokumana ndi mavuto, pokhala opanda zinthu zofunika, pokumana ndi zinthu zovuta,+ 5 pomenyedwa, kuikidwa mʼndende,+ zipolowe, pogwira ntchito mwakhama, kusagona tulo ndiponso kukhala osadya.+
-