Salimo 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale ndikuyenda mʼchigwa chamdima wandiweyani,+Sindikuopa kanthu,+Chifukwa inu muli ndi ine.+Chibonga chanu ndi ndodo yanu zikundipangitsa kumva kuti ndine wotetezeka.* 2 Akorinto 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe Mulungu, amene amalimbikitsa anthu amene ali ndi nkhawa,+ anatilimbikitsa ndi kubwera kwa Tito.
4 Ngakhale ndikuyenda mʼchigwa chamdima wandiweyani,+Sindikuopa kanthu,+Chifukwa inu muli ndi ine.+Chibonga chanu ndi ndodo yanu zikundipangitsa kumva kuti ndine wotetezeka.*
6 Komabe Mulungu, amene amalimbikitsa anthu amene ali ndi nkhawa,+ anatilimbikitsa ndi kubwera kwa Tito.