Aroma 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndikuona kuti mavuto amene tikukumana nawo panopa ndi aangʼono powayerekezera ndi ulemerero umene udzaonekere kudzera mwa ife.+ 2 Timoteyo 2:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawu awa ndi oona: Ndithudi, ngati tinafa naye limodzi, tidzakhalanso ndi moyo limodzi naye.+ 12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso naye monga mafumu.+ Tikamukana, iyenso adzatikana,+
18 Ndikuona kuti mavuto amene tikukumana nawo panopa ndi aangʼono powayerekezera ndi ulemerero umene udzaonekere kudzera mwa ife.+
11 Mawu awa ndi oona: Ndithudi, ngati tinafa naye limodzi, tidzakhalanso ndi moyo limodzi naye.+ 12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso naye monga mafumu.+ Tikamukana, iyenso adzatikana,+