1 Akorinto 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ife timalalikira za Khristu amene anaphedwa popachikidwa pamtengo wozunzikirapo.* Ayuda amaona kuti zimenezi nʼzokhumudwitsa ndipo anthu a mitundu ina amaona kuti nʼzopusa.+
23 Koma ife timalalikira za Khristu amene anaphedwa popachikidwa pamtengo wozunzikirapo.* Ayuda amaona kuti zimenezi nʼzokhumudwitsa ndipo anthu a mitundu ina amaona kuti nʼzopusa.+