Akolose 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Sakutsatira amene ndi mutu,+ amene kudzera mwa iye, thupi lonse limapeza zonse zimene limafunikira ndipo ziwalo zake ndi zolumikizana bwino ndi mfundo zake komanso minyewa ndipo limakulabe mothandizidwa ndi Mulungu.+
19 Sakutsatira amene ndi mutu,+ amene kudzera mwa iye, thupi lonse limapeza zonse zimene limafunikira ndipo ziwalo zake ndi zolumikizana bwino ndi mfundo zake komanso minyewa ndipo limakulabe mothandizidwa ndi Mulungu.+