Yakobo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho gonjerani Mulungu,+ koma tsutsani Mdyerekezi+ ndipo adzakuthawani.+