2 Akorinto 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma tikusonyeza mʼnjira iliyonse kuti ndife atumiki a Mulungu.+ Tikuchita zimenezi popirira zinthu zambiri, pokumana ndi mavuto, pokhala opanda zinthu zofunika, pokumana ndi zinthu zovuta,+ 2 Akorinto 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 polankhula zoona ndiponso pokhala ndi mphamvu ya Mulungu.+ Komanso tikuchita zimenezi ponyamula zida za chilungamo+ kudzanja lamanja* ndi lamanzere,*
4 Koma tikusonyeza mʼnjira iliyonse kuti ndife atumiki a Mulungu.+ Tikuchita zimenezi popirira zinthu zambiri, pokumana ndi mavuto, pokhala opanda zinthu zofunika, pokumana ndi zinthu zovuta,+
7 polankhula zoona ndiponso pokhala ndi mphamvu ya Mulungu.+ Komanso tikuchita zimenezi ponyamula zida za chilungamo+ kudzanja lamanja* ndi lamanzere,*