Mateyu 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yesu anayandikira nʼkuwauza kuti: “Ulamuliro wonse waperekedwa kwa ine kumwamba ndi padziko lapansi.+ Aefeso 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 chifukwa mwamuna ndi mutu wa mkazi wake+ mofanana ndi Khristu amene ndi mutu wa mpingo,+ popeza iye ndi mpulumutsi wa thupi* limeneli. Akolose 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye ndi mutu wa thupi, lomwe ndi mpingo.+ Iye ndi chiyambi, woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,+ kuti adzakhale woyamba pa zinthu zonse.
18 Tsopano Yesu anayandikira nʼkuwauza kuti: “Ulamuliro wonse waperekedwa kwa ine kumwamba ndi padziko lapansi.+
23 chifukwa mwamuna ndi mutu wa mkazi wake+ mofanana ndi Khristu amene ndi mutu wa mpingo,+ popeza iye ndi mpulumutsi wa thupi* limeneli.
18 Iye ndi mutu wa thupi, lomwe ndi mpingo.+ Iye ndi chiyambi, woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,+ kuti adzakhale woyamba pa zinthu zonse.