2 Akorinto 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso, Mulungu akhoza kukusonyezani kwambiri kukoma mtima kwake kwakukulu kuti musasowe zinthu zofunika pa moyo komanso kuti mukhale ndi zinthu zambiri zokuthandizani kugwira ntchito iliyonse yabwino.+
8 Komanso, Mulungu akhoza kukusonyezani kwambiri kukoma mtima kwake kwakukulu kuti musasowe zinthu zofunika pa moyo komanso kuti mukhale ndi zinthu zambiri zokuthandizani kugwira ntchito iliyonse yabwino.+