Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano ndikukudandaulirani abale, mʼdzina la Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti nonse muzilankhula mogwirizana ndipo pakati panu pasakhale kugawanika,+ koma mukhale ogwirizana kwambiri pokhala ndi mtima umodzi ndi maganizo amodzi.+

  • 2 Akorinto 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pomaliza abale, pitirizani kusangalala, kusintha maganizo, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu amene ndi wachikondi komanso wamtendere+ adzakhala nanu.

  • 1 Petulo 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pomaliza, nonsenu mukhale amaganizo amodzi,+ muzimverana chisoni, muzikonda abale, mukhale ndi chifundo chachikulu+ ndiponso mukhale odzichepetsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena