Agalatiya 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tisakhale odzikuza,+ tisamayambitse mpikisano pakati pathu+ komanso tisamachitirane kaduka.