Agalatiya 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Khristu anatigula+ nʼkutimasula+ ku temberero la Chilamulo. Anachita zimenezi pokhala temberero mʼmalo mwa ife, chifukwa Malemba amati: “Munthu aliyense wopachikidwa pamtengo ndi wotembereredwa.”+
13 Khristu anatigula+ nʼkutimasula+ ku temberero la Chilamulo. Anachita zimenezi pokhala temberero mʼmalo mwa ife, chifukwa Malemba amati: “Munthu aliyense wopachikidwa pamtengo ndi wotembereredwa.”+