Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+ 1 Petulo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 inunso monga miyala yamoyo mukumangidwa nʼkukhala nyumba yauzimu+ kuti mudzakhale ansembe oyera. Monga ansembe oyera muzidzapereka nsembe zauzimu+ zovomerezeka pamaso pa Mulungu kudzera mwa Yesu Khristu.+
15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+
5 inunso monga miyala yamoyo mukumangidwa nʼkukhala nyumba yauzimu+ kuti mudzakhale ansembe oyera. Monga ansembe oyera muzidzapereka nsembe zauzimu+ zovomerezeka pamaso pa Mulungu kudzera mwa Yesu Khristu.+