Filimoni 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndikukupempha za mwana wanga Onesimo,+ amene ndakhala bambo wake+ pamene ndili kundende kuno. Filimoni 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikanakonda kukhala nayebe kuti mʼmalo mwa iwe, apitirize kunditumikira pamene ndili kundende kuno chifukwa cha uthenga wabwino.+
13 Ndikanakonda kukhala nayebe kuti mʼmalo mwa iwe, apitirize kunditumikira pamene ndili kundende kuno chifukwa cha uthenga wabwino.+