Yohane 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pa tsiku limenelo simudzandifunsanso mafunso. Ndithudi ndikukuuzani, ngati mungapemphe chilichonse kwa Atate+ mʼdzina langa adzakupatsani.+ Aroma 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kondwerani chifukwa cha chiyembekezo. Muzipirira mavuto.+ Muzilimbikira kupemphera.+ 1 Petulo 5:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho dzichepetseni pamaso pa Mulungu wathu wamphamvu* kuti adzakukwezeni nthawi yake ikadzakwana.+ 7 Muzichita zimenezi pamene mukumutulira nkhawa zanu zonse,+ chifukwa amakufunirani zabwino.+
23 Pa tsiku limenelo simudzandifunsanso mafunso. Ndithudi ndikukuuzani, ngati mungapemphe chilichonse kwa Atate+ mʼdzina langa adzakupatsani.+
6 Choncho dzichepetseni pamaso pa Mulungu wathu wamphamvu* kuti adzakukwezeni nthawi yake ikadzakwana.+ 7 Muzichita zimenezi pamene mukumutulira nkhawa zanu zonse,+ chifukwa amakufunirani zabwino.+