Akolose 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso lolani kuti mtendere wa Khristu ulamulire mʼmitima yanu,+ popeza munaitanidwa ku mtendere umenewu monga ziwalo za thupi limodzi. Ndipo sonyezani kuti ndinu oyamikira. 1 Atesalonika 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzithokoza pa chilichonse.+ Mulungu akufuna kuti muzichita zimenezi chifukwa ndinu otsatira a Khristu Yesu.
15 Komanso lolani kuti mtendere wa Khristu ulamulire mʼmitima yanu,+ popeza munaitanidwa ku mtendere umenewu monga ziwalo za thupi limodzi. Ndipo sonyezani kuti ndinu oyamikira.
18 Muzithokoza pa chilichonse.+ Mulungu akufuna kuti muzichita zimenezi chifukwa ndinu otsatira a Khristu Yesu.