Aroma 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho abale, ndikukupemphani kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu komanso chikondi cha mzimu, kuti muzilimbikira kundipempherera kwa Mulungu ndipo nanenso ndikulimbikira kupemphera.+
30 Choncho abale, ndikukupemphani kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu komanso chikondi cha mzimu, kuti muzilimbikira kundipempherera kwa Mulungu ndipo nanenso ndikulimbikira kupemphera.+