Akolose 1:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zimenezi ndi zimene munaphunzira kwa Epafura,+ kapolo mnzathu wokondedwa, amene ndi mtumiki wokhulupirika wa Khristu mʼmalo mwa ife. 8 Iye ndi amenenso anatidziwitsa za chikondi chanu chimene munachisonyeza mothandizidwa ndi mzimu wa Mulungu.*
7 Zimenezi ndi zimene munaphunzira kwa Epafura,+ kapolo mnzathu wokondedwa, amene ndi mtumiki wokhulupirika wa Khristu mʼmalo mwa ife. 8 Iye ndi amenenso anatidziwitsa za chikondi chanu chimene munachisonyeza mothandizidwa ndi mzimu wa Mulungu.*