-
Afilipi 1:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Nʼzoyenera kwa ine kuti ndiganizire nonsenu mwa njira imeneyi, chifukwa ndinu apamtima panga. Inu amene munandithandiza pa nthawi imene ndinamangidwa maunyolo mʼndende+ komanso poteteza uthenga wabwino ndi kukhazikitsa mwalamulo ntchito yolengeza uthenga wabwino.+ Inu limodzi ndi ine tinapindula ndi kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu.
-
-
Filimoni 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 ndikuona kuti ndi bwino ndichite kukupempha mwachikondi. Ineyo Paulo, amene ndine wachikulire komanso mkaidi chifukwa cha Khristu Yesu,
-