Aefeso 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 mpaka tonse tidzakhale ogwirizana pa zimene timakhulupirira komanso podziwa molondola Mwana wa Mulungu. Zikadzatero, tidzakhala anthu achikulire, amene afika pa msinkhu wa munthu wamkulu+ ngati mmene Khristu analili.
13 mpaka tonse tidzakhale ogwirizana pa zimene timakhulupirira komanso podziwa molondola Mwana wa Mulungu. Zikadzatero, tidzakhala anthu achikulire, amene afika pa msinkhu wa munthu wamkulu+ ngati mmene Khristu analili.