1 Akorinto 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma inu ndinu ogwirizana ndi Khristu Yesu chifukwa cha Mulunguyo. Yesuyo amatisonyeza nzeru za Mulungu ndiponso chilungamo cha Mulungu.+ Kudzera mwa Yesu, anthu akhoza kuyeretsedwa,+ ndipo kudzera mwa dipo* akhoza kumasulidwa,+ 1 Akorinto 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nanga “ndani akudziwa maganizo a Yehova* kuti amulangize?”+ Koma ife tili ndi maganizo a Khristu.+
30 Koma inu ndinu ogwirizana ndi Khristu Yesu chifukwa cha Mulunguyo. Yesuyo amatisonyeza nzeru za Mulungu ndiponso chilungamo cha Mulungu.+ Kudzera mwa Yesu, anthu akhoza kuyeretsedwa,+ ndipo kudzera mwa dipo* akhoza kumasulidwa,+
16 Nanga “ndani akudziwa maganizo a Yehova* kuti amulangize?”+ Koma ife tili ndi maganizo a Khristu.+