Aroma 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho tinaikidwa naye limodzi mʼmanda pamene tinabatizidwa mu imfa yake,+ kuti mofanana ndi Khristu amene anaukitsidwa kudzera mu ulemerero wa Atate, ifenso tikhale moyo watsopano.+
4 Choncho tinaikidwa naye limodzi mʼmanda pamene tinabatizidwa mu imfa yake,+ kuti mofanana ndi Khristu amene anaukitsidwa kudzera mu ulemerero wa Atate, ifenso tikhale moyo watsopano.+