Aefeso 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuwonjezera pamenepo, Mulungu anatichititsa kuti tikhale ndi moyo ndipo anatipatsa malo oti tikakhale kumwamba chifukwa anatigwirizanitsa ndi Khristu Yesu.+ Akolose 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komabe, ngati munaukitsidwa limodzi ndi Khristu,+ pitirizani kufunafuna zinthu zakumwamba, kumene Khristu wakhala kudzanja lamanja la Mulungu.+
6 Kuwonjezera pamenepo, Mulungu anatichititsa kuti tikhale ndi moyo ndipo anatipatsa malo oti tikakhale kumwamba chifukwa anatigwirizanitsa ndi Khristu Yesu.+
3 Komabe, ngati munaukitsidwa limodzi ndi Khristu,+ pitirizani kufunafuna zinthu zakumwamba, kumene Khristu wakhala kudzanja lamanja la Mulungu.+