Aefeso 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuwonjezera pamenepo, Mulungu anapangitsa kuti mukhale amoyo ngakhale kuti munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu komanso machimo anu.+ Aefeso 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 anapangitsa kuti tikhale amoyo limodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa chifukwa cha machimo athu,+ ndipotu inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu.
2 Kuwonjezera pamenepo, Mulungu anapangitsa kuti mukhale amoyo ngakhale kuti munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu komanso machimo anu.+
5 anapangitsa kuti tikhale amoyo limodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa chifukwa cha machimo athu,+ ndipotu inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu.